Yesaya 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye adzatambasula manja ake n’kuwamenyetsa pakati pa mzindawo ngati mmene munthu wosambira amatambasulira manja ake n’kuwamenyetsa pamadzi akamasambira. Adzathetsa kunyada+ kwa mzindawo poumenya mwaluso ndi manja ake. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:11 Yesaya 1, ptsa. 274-276
11 Iye adzatambasula manja ake n’kuwamenyetsa pakati pa mzindawo ngati mmene munthu wosambira amatambasulira manja ake n’kuwamenyetsa pamadzi akamasambira. Adzathetsa kunyada+ kwa mzindawo poumenya mwaluso ndi manja ake.