Yesaya 26:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo afa. Sadzakhalanso ndi moyo.+ Iwo ndi akufa+ ndipo sadzaukanso.+ Pa chifukwa chimenechi, mwawatembenukira kuti muwawononge n’cholinga choti asadzatchulidwenso.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:14 Nsanja ya Olonda,3/1/2001, tsa. 20 Yesaya 1, tsa. 281
14 Iwo afa. Sadzakhalanso ndi moyo.+ Iwo ndi akufa+ ndipo sadzaukanso.+ Pa chifukwa chimenechi, mwawatembenukira kuti muwawononge n’cholinga choti asadzatchulidwenso.+