Yesaya 26:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chifukwa cha inu Yehova, ife takhala ngati mkazi wapakati amene watsala pang’ono kubereka, amene akumva zowawa za pobereka, amene akulira ndi ululu wa pobereka.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:17 Nsanja ya Olonda,3/1/2001, tsa. 20 Yesaya 1, tsa. 282
17 Chifukwa cha inu Yehova, ife takhala ngati mkazi wapakati amene watsala pang’ono kubereka, amene akumva zowawa za pobereka, amene akulira ndi ululu wa pobereka.+