Yesaya 32:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Panthaka ya anthu anga, pakungomera zitsamba zaminga.+ Zamera panyumba zonse zimene kale zinali zodzaza ndi chisangalalo. Zamera m’tauni imene kale inali yodzaza ndi chikondwerero.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:13 Yesaya 1, tsa. 339
13 Panthaka ya anthu anga, pakungomera zitsamba zaminga.+ Zamera panyumba zonse zimene kale zinali zodzaza ndi chisangalalo. Zamera m’tauni imene kale inali yodzaza ndi chikondwerero.+