Yesaya 38:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 M’malo mopeza mtendere ndinapeza zowawa, zowawatu zedi!+Inuyo mwamamatira moyo wanga ndipo mwauteteza kuti usapite kudzenje la chiwonongeko.+Pakuti machimo anga onse mwawaponyera kumbuyo kwanu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 38:17 Yandikirani, tsa. 264 Nsanja ya Olonda,7/1/2003, tsa. 18
17 M’malo mopeza mtendere ndinapeza zowawa, zowawatu zedi!+Inuyo mwamamatira moyo wanga ndipo mwauteteza kuti usapite kudzenje la chiwonongeko.+Pakuti machimo anga onse mwawaponyera kumbuyo kwanu.+