Yesaya 41:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu amene akulimbana nawe udzawafunafuna koma sudzawapeza. Anthu amene akumenyana nawe+ adzakhala ngati kulibeko ndipo sadzakhalanso ngati kanthu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 41:12 Yesaya 2, ptsa. 23-24
12 Anthu amene akulimbana nawe udzawafunafuna koma sudzawapeza. Anthu amene akumenyana nawe+ adzakhala ngati kulibeko ndipo sadzakhalanso ngati kanthu.+