Yesaya 42:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Imbirani Yehova nyimbo yatsopano.+ M’tamandeni kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+ M’tamandeni inu amuna amene mumadalira nyanja+ ndi zonse zokhala mmenemo, ndiponso inu zilumba ndi anthu okhala m’zilumbazo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 42:10 Nsanja ya Olonda,12/15/2001, tsa. 25 Yesaya 2, ptsa. 41-42
10 Imbirani Yehova nyimbo yatsopano.+ M’tamandeni kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+ M’tamandeni inu amuna amene mumadalira nyanja+ ndi zonse zokhala mmenemo, ndiponso inu zilumba ndi anthu okhala m’zilumbazo.+