Yesaya 42:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chipululu+ ndi mizinda ya kumeneko, ndiponso midzi ya ku Kedara zikweze mawu awo.+ Anthu okhala m’dera lamatanthwe+ afuule mokondwera. Anthu afuule kuchokera pamwamba pa mapiri. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 42:11 Yesaya 2, ptsa. 41-42
11 Chipululu+ ndi mizinda ya kumeneko, ndiponso midzi ya ku Kedara zikweze mawu awo.+ Anthu okhala m’dera lamatanthwe+ afuule mokondwera. Anthu afuule kuchokera pamwamba pa mapiri.