Yesaya 42:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu amene akudalira zifaniziro zosema, amene akuuza zifaniziro zopangidwa ndi chitsulo chosungunula kuti: “Ndinu milungu yathu,” adzathawa ndipo adzachita manyazi kwambiri.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 42:17 Yesaya 2, tsa. 44
17 Anthu amene akudalira zifaniziro zosema, amene akuuza zifaniziro zopangidwa ndi chitsulo chosungunula kuti: “Ndinu milungu yathu,” adzathawa ndipo adzachita manyazi kwambiri.+