Yesaya 42:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndani amene ali wakhungu? Mtumiki wanga ndiye wakhungu. Ndani amene ali wogontha ngati mtumiki wanga amene ndamutuma? Ndani amene ali wakhungu ngati munthu amene wapatsidwa mphoto, kapena amene ali wakhungu ngati mtumiki wa Yehova?+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 42:19 Yesaya 2, ptsa. 44-45
19 Ndani amene ali wakhungu? Mtumiki wanga ndiye wakhungu. Ndani amene ali wogontha ngati mtumiki wanga amene ndamutuma? Ndani amene ali wakhungu ngati munthu amene wapatsidwa mphoto, kapena amene ali wakhungu ngati mtumiki wa Yehova?+