Yesaya 44:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthu onse opanga zifaniziro zosema ndi opanda pake,+ ndipo mafano awo okondedwa adzakhala opanda phindu.+ Monga mboni zawo, mafanowo saona chilichonse ndipo sadziwa chilichonse,+ kuti anthu opanga mafanowo achite manyazi.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 44:9 Yesaya 2, tsa. 66
9 Anthu onse opanga zifaniziro zosema ndi opanda pake,+ ndipo mafano awo okondedwa adzakhala opanda phindu.+ Monga mboni zawo, mafanowo saona chilichonse ndipo sadziwa chilichonse,+ kuti anthu opanga mafanowo achite manyazi.+