14 Pali munthu amene ntchito yake ndi yogwetsa mitengo ya mkungudza. Iye amasankha mtengo wamtundu winawake, waukulu kwambiri, n’kuusiya kuti ukule n’kukhwima pakati pa mitengo ya m’nkhalango.+ Iye anabzala mtengo wa paini, ndipo mvula yaukulitsa kwambiri.