Yesaya 44:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Yehova, Wokuwombola+ ndiponso amene anakuumba kuyambira uli m’mimba, wanena kuti: “Ine Yehova ndachita zonse. Ndinatambasula ndekha kumwamba,+ ndi kukhazikitsa dziko lapansi.+ Kodi ndani anali nane? Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 44:24 Yesaya 2, ptsa. 70-71
24 Yehova, Wokuwombola+ ndiponso amene anakuumba kuyambira uli m’mimba, wanena kuti: “Ine Yehova ndachita zonse. Ndinatambasula ndekha kumwamba,+ ndi kukhazikitsa dziko lapansi.+ Kodi ndani anali nane?