Yesaya 47:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano imirira, tenga nyanga zako ndiponso zamatsenga zako zambirimbiri+ zomwe wazivutikira kuyambira uli mwana. Uzitenge kuti mwina zingakuthandize kapenanso kuti ungachite nazo zodabwitsa kwa anthu. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 47:12 Yesaya 2, ptsa. 113-114
12 Tsopano imirira, tenga nyanga zako ndiponso zamatsenga zako zambirimbiri+ zomwe wazivutikira kuyambira uli mwana. Uzitenge kuti mwina zingakuthandize kapenanso kuti ungachite nazo zodabwitsa kwa anthu.