Yesaya 48:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Ndanena zinthu zoyambirira kuchokera pa nthawi imeneyo. Zinatuluka pakamwa panga, ndipo ndinazichititsa kumveka.+ Mwadzidzidzi, ndinazichita ndipo zinachitikadi.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 48:3 Yesaya 2, ptsa. 123, 125
3 “Ndanena zinthu zoyambirira kuchokera pa nthawi imeneyo. Zinatuluka pakamwa panga, ndipo ndinazichititsa kumveka.+ Mwadzidzidzi, ndinazichita ndipo zinachitikadi.+