Yesaya 51:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti njenjete idzawadya ngati chovala ndipo kachilombo kodya zovala kadzawadya ngati thonje.+ Koma chilungamo changa chidzakhala mpaka kalekale ndipo chipulumutso changa chidzafikira mibadwo yosawerengeka.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 51:8 Yesaya 2, ptsa. 171-172
8 Pakuti njenjete idzawadya ngati chovala ndipo kachilombo kodya zovala kadzawadya ngati thonje.+ Koma chilungamo changa chidzakhala mpaka kalekale ndipo chipulumutso changa chidzafikira mibadwo yosawerengeka.”+