54 “Iwe mkazi wosabereka amene sunaberekepo mwana,+ fuula mokondwa!+ Iwe amene sunamvepo zowawa za pobereka,+ kondwera! Fuula mokondwa! Kuwa ndi chisangalalo, pakuti ana a mkazi wosiyidwa ndi ambiri kuposa ana a mkazi yemwe ali ndi mwamuna,”+ watero Yehova.