Yesaya 57:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwe unatsetserekera kwa Meleki utatenga mafuta, ndipo unachulukitsa mafuta ako onunkhira.+ Unapitiriza kutumiza nthumwi zako kutali kwambiri moti mpaka unatsitsira zochita zako m’Manda.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 57:9 Yesaya 2, ptsa. 266-268
9 Iwe unatsetserekera kwa Meleki utatenga mafuta, ndipo unachulukitsa mafuta ako onunkhira.+ Unapitiriza kutumiza nthumwi zako kutali kwambiri moti mpaka unatsitsira zochita zako m’Manda.+