Yesaya 61:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti monga momwe dziko lapansi limatulutsira zomera zake, ndiponso monga momwe munda umameretsera zinthu zimene zabzalidwa mmenemo,+ momwemonso Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzameretsa chilungamo+ ndi chitamando pamaso pa mitundu yonse.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 61:11 Yesaya 2, ptsa. 333-334 Nsanja ya Olonda,1/1/1993, ptsa. 9-10
11 Pakuti monga momwe dziko lapansi limatulutsira zomera zake, ndiponso monga momwe munda umameretsera zinthu zimene zabzalidwa mmenemo,+ momwemonso Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzameretsa chilungamo+ ndi chitamando pamaso pa mitundu yonse.+