Yesaya 63:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 N’chifukwa chiyani inu Yehova mukutichititsa kuchoka panjira zanu? N’chifukwa chiyani mukuumitsa mtima wathu kuti tisakuopeni?+ Bwererani chifukwa cha atumiki anu, mafuko a cholowa chanu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 63:17 Yesaya 2, ptsa. 361-363
17 N’chifukwa chiyani inu Yehova mukutichititsa kuchoka panjira zanu? N’chifukwa chiyani mukuumitsa mtima wathu kuti tisakuopeni?+ Bwererani chifukwa cha atumiki anu, mafuko a cholowa chanu.+