Yesaya 65:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 chifukwa cha zolakwa zawo ndi zolakwa za makolo awo pa nthawi imodzi,”+ watero Yehova. “Popeza afukiza nsembe zautsi pamapiri ndipo andinyoza+ pazitunda,+ ine ndidzawayezera mphoto yawo choyamba, n’kuiika pachifuwa pawo.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 65:7 Yesaya 2, ptsa. 375-376
7 chifukwa cha zolakwa zawo ndi zolakwa za makolo awo pa nthawi imodzi,”+ watero Yehova. “Popeza afukiza nsembe zautsi pamapiri ndipo andinyoza+ pazitunda,+ ine ndidzawayezera mphoto yawo choyamba, n’kuiika pachifuwa pawo.”+