Yesaya 65:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anthu inu mudzasiya dzina lanu kuti anthu anga osankhidwa mwapadera aziligwiritsa ntchito potemberera ndipo Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzakuphani mmodzi ndi mmodzi,+ koma atumiki ake adzawapatsa dzina lina.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 65:15 Yesaya 2, ptsa. 380-381
15 Anthu inu mudzasiya dzina lanu kuti anthu anga osankhidwa mwapadera aziligwiritsa ntchito potemberera ndipo Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzakuphani mmodzi ndi mmodzi,+ koma atumiki ake adzawapatsa dzina lina.+