Yesaya 66:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mkazi anabereka asanayambe kumva zowawa za pobereka.+ Ululu wa pobereka usanamubwerere, iye anabereka mwana wamwamuna.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 66:7 Yesaya 2, ptsa. 397-398 Nsanja ya Olonda,1/1/1995, tsa. 11
7 Mkazi anabereka asanayambe kumva zowawa za pobereka.+ Ululu wa pobereka usanamubwerere, iye anabereka mwana wamwamuna.+