Yeremiya 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Kodi ndilankhule ndi ndani ndipo ndichenjeze ndani kuti amve? Taonani! Makutu awo sanawachite mdulidwe, moti sangamve.+ Taonani! Mawu a Yehova akhala onyozeka kwa iwo,+ ndipo sakukondwera nawo.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:10 Nsanja ya Olonda,4/1/1988, tsa. 18
10 “Kodi ndilankhule ndi ndani ndipo ndichenjeze ndani kuti amve? Taonani! Makutu awo sanawachite mdulidwe, moti sangamve.+ Taonani! Mawu a Yehova akhala onyozeka kwa iwo,+ ndipo sakukondwera nawo.+