Yeremiya 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti imfa yatilowera m’nyumba kudzera m’mawindo. Yalowa munsanja zathu zokhalamo kuti mumsewu musapezeke mwana aliyense ndiponso kuti anyamata asapezeke m’mabwalo a mzinda.’+
21 Pakuti imfa yatilowera m’nyumba kudzera m’mawindo. Yalowa munsanja zathu zokhalamo kuti mumsewu musapezeke mwana aliyense ndiponso kuti anyamata asapezeke m’mabwalo a mzinda.’+