Yeremiya 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsoka ine chifukwa cha kuwonongedwa kwanga!+ Chilonda changa cha mkwapulo chakhala chosachiritsika. Ndipo ndanena kuti: “Ndithudi amenewa ndi matenda anga ndipo ndidzakhalabe nawo.+
19 Tsoka ine chifukwa cha kuwonongedwa kwanga!+ Chilonda changa cha mkwapulo chakhala chosachiritsika. Ndipo ndanena kuti: “Ndithudi amenewa ndi matenda anga ndipo ndidzakhalabe nawo.+