Yeremiya 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Abusa achita zinthu mopanda nzeru,+ ndipo sanayese n’komwe kufunafuna Yehova.+ N’chifukwa chake sanachite zinthu mozindikira, ndipo ziweto zawo zonse zabalalika.”+
21 Abusa achita zinthu mopanda nzeru,+ ndipo sanayese n’komwe kufunafuna Yehova.+ N’chifukwa chake sanachite zinthu mozindikira, ndipo ziweto zawo zonse zabalalika.”+