Yeremiya 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Kodi anthu anga okondedwa akufuna chiyani m’nyumba yanga+ pamene ambiri a iwo akuchita zoipa zoterezi?+ Kodi nyama yopatulika imene amaipereka nsembe idzawapulumutsa tsoka lawo likadzafika?+ Kodi iwo adzakondwera pa nthawi imeneyo?+
15 “Kodi anthu anga okondedwa akufuna chiyani m’nyumba yanga+ pamene ambiri a iwo akuchita zoipa zoterezi?+ Kodi nyama yopatulika imene amaipereka nsembe idzawapulumutsa tsoka lawo likadzafika?+ Kodi iwo adzakondwera pa nthawi imeneyo?+