Yeremiya 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma Yehova wa makamu amaweruza mwachilungamo.+ Amafufuza impso ndi mtima.+ Inu Mulungu, ndiloleni ndione mukuwapatsa chilango, pakuti ine ndakufotokozerani mlandu wanga.+
20 Koma Yehova wa makamu amaweruza mwachilungamo.+ Amafufuza impso ndi mtima.+ Inu Mulungu, ndiloleni ndione mukuwapatsa chilango, pakuti ine ndakufotokozerani mlandu wanga.+