Yeremiya 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamene akusala kudya ine sindikumvetsera kuchonderera kwawo.+ Pamene akupereka nsembe zopsereza zathunthu ndi nsembe zambewu ine sindikukondwera nazo,+ ndipo ndiwawononga ndi lupanga, njala yaikulu ndiponso mliri.”+
12 Pamene akusala kudya ine sindikumvetsera kuchonderera kwawo.+ Pamene akupereka nsembe zopsereza zathunthu ndi nsembe zambewu ine sindikukondwera nazo,+ ndipo ndiwawononga ndi lupanga, njala yaikulu ndiponso mliri.”+