Yeremiya 25:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo musatsatire milungu ina kuti muziitumikira ndi kuigwadira. Mukachita zimenezo mudzandikhumudwitsa chifukwa cha mafano anu amene mudzapanga, ndipo ineyo ndidzakugwetserani tsoka.’+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:6 Nsanja ya Olonda,3/1/1994, tsa. 19
6 Ndipo musatsatire milungu ina kuti muziitumikira ndi kuigwadira. Mukachita zimenezo mudzandikhumudwitsa chifukwa cha mafano anu amene mudzapanga, ndipo ineyo ndidzakugwetserani tsoka.’+