Yeremiya 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno m’chaka chimenecho, chaka chachinayi, m’mwezi wachisanu, kuchiyambi kwa ufumu wa Zedekiya+ mfumu ya Yuda, Hananiya+ mwana wa Azuri, mneneri wa ku Gibeoni,+ anauza Yeremiya m’nyumba ya Yehova pamaso pa ansembe ndi anthu onse kuti:
28 Ndiyeno m’chaka chimenecho, chaka chachinayi, m’mwezi wachisanu, kuchiyambi kwa ufumu wa Zedekiya+ mfumu ya Yuda, Hananiya+ mwana wa Azuri, mneneri wa ku Gibeoni,+ anauza Yeremiya m’nyumba ya Yehova pamaso pa ansembe ndi anthu onse kuti: