6 inde, Yeremiya anayankha kuti: “Zikhale momwemo!+ Yehova achitedi zimenezo! Yehova akwaniritse zonse zimene walosera m’mawu ako. Achite zimenezo mwa kubwezeretsa pamalo ano ziwiya za m’nyumba ya Yehova ndi anthu onse amene anatengedwa kupita ku ukapolo ku Babulo!+