Yeremiya 34:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma pambuyo pake, iwo anatembenuka+ ndi kuyamba kutenganso amuna ndi akazi antchitowo amene anawalola kupita kwawo mwaufulu ndipo anayamba kuwagwiritsa ntchito monga antchito awo aamuna ndi aakazi.+
11 Koma pambuyo pake, iwo anatembenuka+ ndi kuyamba kutenganso amuna ndi akazi antchitowo amene anawalola kupita kwawo mwaufulu ndipo anayamba kuwagwiritsa ntchito monga antchito awo aamuna ndi aakazi.+