Yeremiya 35:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma iwo anati: “Sitingamwe vinyo, chifukwa Yonadabu mwana wa Rekabu,+ kholo lathu, anatilamula kuti, ‘Inuyo kapena ana anu musamamwe vinyo mpaka kalekale.+
6 Koma iwo anati: “Sitingamwe vinyo, chifukwa Yonadabu mwana wa Rekabu,+ kholo lathu, anatilamula kuti, ‘Inuyo kapena ana anu musamamwe vinyo mpaka kalekale.+