Yeremiya 35:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma pamene Nebukadirezara mfumu ya Babulo anabwera kudzaukira dzikoli+ tinati, ‘Tiyeni tilowe mu Yerusalemu chifukwa kukubwera magulu ankhondo a Akasidi ndi magulu ankhondo a ku Siriya. Tiyeni tikakhale mu Yerusalemu.’”+
11 Koma pamene Nebukadirezara mfumu ya Babulo anabwera kudzaukira dzikoli+ tinati, ‘Tiyeni tilowe mu Yerusalemu chifukwa kukubwera magulu ankhondo a Akasidi ndi magulu ankhondo a ku Siriya. Tiyeni tikakhale mu Yerusalemu.’”+