Yeremiya 36:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamenepo Baruki anawauza kuti: “Iye anali kundiuza mawu onsewa ndipo ine ndinali kulemba mumpukutuwu ndi inki.”+
18 Pamenepo Baruki anawauza kuti: “Iye anali kundiuza mawu onsewa ndipo ine ndinali kulemba mumpukutuwu ndi inki.”+