Yeremiya 37:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano ali kuti aneneri anu amene anali kulosera kwa inu ponena kuti, ‘Mfumu ya Babulo sidzabwera kudzamenyana ndi anthu inu ndiponso kudzamenyana ndi dzikoli’?+
19 Tsopano ali kuti aneneri anu amene anali kulosera kwa inu ponena kuti, ‘Mfumu ya Babulo sidzabwera kudzamenyana ndi anthu inu ndiponso kudzamenyana ndi dzikoli’?+