Yeremiya 43:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 moti Yohanani mwana wa Kareya ndi akuluakulu onse a magulu ankhondo anatenga otsala a Yuda amene anabwerera kuchokera ku mitundu yonse ya anthu kumene anathawira kuti akhale m’dziko la Yuda kwa kanthawi kochepa.+
5 moti Yohanani mwana wa Kareya ndi akuluakulu onse a magulu ankhondo anatenga otsala a Yuda amene anabwerera kuchokera ku mitundu yonse ya anthu kumene anathawira kuti akhale m’dziko la Yuda kwa kanthawi kochepa.+