Yeremiya 44:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Tsopano Yehova, Mulungu wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘N’chifukwa chiyani mukudziitanira tsoka lalikulu?+ Kodi simukudziwa kuti muphetsa amuna, akazi, ana aang’ono ndi ana oyamwa+ pakati pa Yuda, moti sipapezeka wotsala aliyense?
7 “Tsopano Yehova, Mulungu wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘N’chifukwa chiyani mukudziitanira tsoka lalikulu?+ Kodi simukudziwa kuti muphetsa amuna, akazi, ana aang’ono ndi ana oyamwa+ pakati pa Yuda, moti sipapezeka wotsala aliyense?