15 Ndiyeno amuna onse amene anali kudziwa kuti akazi awo anali kupereka nsembe zautsi kwa milungu ina,+ akazi onse amene anaimirira ndi kupanga mpingo waukulu, komanso anthu onse amene anali kukhala ku Iguputo+ m’dera la Patirosi,+ anayankha Yeremiya kuti: