Yeremiya 44:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipotu kuyambira pamene tinasiya kupereka nsembe zautsi ndi kuthira nsembe zachakumwa kwa ‘mfumukazi yakumwamba,’+ chilichonse chikutisowa, ndipo tawonongeka chifukwa cha lupanga ndi njala yaikulu.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 44:18 Nsanja ya Olonda,5/15/1999, ptsa. 13-14
18 Ndipotu kuyambira pamene tinasiya kupereka nsembe zautsi ndi kuthira nsembe zachakumwa kwa ‘mfumukazi yakumwamba,’+ chilichonse chikutisowa, ndipo tawonongeka chifukwa cha lupanga ndi njala yaikulu.+