Yeremiya 46:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mitundu ya anthu yamva zochititsa manyazi zimene zakuchitikira+ ndipo kulira kwako kwamveka m’dziko lonse.+ Amuna amphamvu apunthwitsana ndi kugwetsana.+ Onse agwera limodzi.”
12 Mitundu ya anthu yamva zochititsa manyazi zimene zakuchitikira+ ndipo kulira kwako kwamveka m’dziko lonse.+ Amuna amphamvu apunthwitsana ndi kugwetsana.+ Onse agwera limodzi.”