Yeremiya 49:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 “Ndiyeno m’masiku otsiriza+ ndidzasonkhanitsa pamodzi anthu a ku Elamu amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina,”+ watero Yehova.
39 “Ndiyeno m’masiku otsiriza+ ndidzasonkhanitsa pamodzi anthu a ku Elamu amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina,”+ watero Yehova.