Yeremiya 50:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Yehova watsegula nkhokwe yake ya zida ndipo akutulutsamo zida zake zodzudzulira mwamphamvu.+ Akutero chifukwa chakuti Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa,+ ali ndi ntchito yoti achite m’dziko la Akasidi.+
25 “Yehova watsegula nkhokwe yake ya zida ndipo akutulutsamo zida zake zodzudzulira mwamphamvu.+ Akutero chifukwa chakuti Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa,+ ali ndi ntchito yoti achite m’dziko la Akasidi.+