Yeremiya 50:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Yehova wa makamu wanena kuti: “Ana a Isiraeli ndi ana a Yuda, onse akuponderezedwa. Anthu onse amene agwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina akuwakakamira+ ndipo sakuwalola kubwerera kwawo.+
33 Yehova wa makamu wanena kuti: “Ana a Isiraeli ndi ana a Yuda, onse akuponderezedwa. Anthu onse amene agwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina akuwakakamira+ ndipo sakuwalola kubwerera kwawo.+