Maliro 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndikulirira zinthu zimenezi ngati mkazi.+ Maso anga ine! Maso anga akutuluka misozi.+Pakuti wonditonthoza, munthu woti anditsitsimule, ali kutali ndi ine.Ana anga asiyidwa+ popanda thandizo, pakuti mdani wanga wadzitukumula.+
16 Ndikulirira zinthu zimenezi ngati mkazi.+ Maso anga ine! Maso anga akutuluka misozi.+Pakuti wonditonthoza, munthu woti anditsitsimule, ali kutali ndi ine.Ana anga asiyidwa+ popanda thandizo, pakuti mdani wanga wadzitukumula.+