Ezekieli 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndikamalankhula nawe ndizikutsegula pakamwa. Ndiyeno iweyo uzikawauza kuti,+ ‘Izi n’zimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena.’ Wakumva amve,+ ndipo wosamva asamve, pakuti iwo ndi nyumba yopanduka.+
27 Ndikamalankhula nawe ndizikutsegula pakamwa. Ndiyeno iweyo uzikawauza kuti,+ ‘Izi n’zimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena.’ Wakumva amve,+ ndipo wosamva asamve, pakuti iwo ndi nyumba yopanduka.+