Ezekieli 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 mwakuti chakudya ndi madzi zidzakhala zosowa. Azidzayang’anizana modabwa ndipo adzaonda chifukwa cha zolakwa zawo.+
17 mwakuti chakudya ndi madzi zidzakhala zosowa. Azidzayang’anizana modabwa ndipo adzaonda chifukwa cha zolakwa zawo.+