Ezekieli 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Iwe mwana wa munthu, tenga lupanga lakuthwa. Likhale ngati lezala lako lometela ndipo umetele tsitsi lako ndi ndevu zako.+ Kenako utenge sikelo yoyezera ndipo ugawe tsitsilo m’magawo atatu. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:1 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, ptsa. 12-13
5 “Iwe mwana wa munthu, tenga lupanga lakuthwa. Likhale ngati lezala lako lometela ndipo umetele tsitsi lako ndi ndevu zako.+ Kenako utenge sikelo yoyezera ndipo ugawe tsitsilo m’magawo atatu.